| Welcome/ Mwalandiridwa/ Welkom |
|
|
Dzina langa ndi Steven Paas, ine ndine katswiri wa mbiri ya mpingo, komanso wofufuza wa Chichewa/ Chinyanja. M’malo mwa Bungwe la Foundation Heart for Malawi ndikulandirani inu ku webusayiti iyi, imene imapatsa nkhani ya Sikimu yathu ya Mtanthauziramawu wa Chichewa/ Chinyanja. Tikuyembekeza kuti msindikizo wachitatu wa dikishonaleyo (CE ndi EC) idzaona kuunika poyamba pa chaka cha 2012. Webusayiti imakhala ndi kapangidwe ka dikishonale kolumikizidwa ndi intaneti, imene imagwiritsidwa ntchito ndi anthu ku dziko lonse lapansi. Komanso pa sayiti tinaonjezera mbiri ya kakhalidwe ka madikishonale a Chichewa/ Chinyanya. Pomaliza tinaphatikizira nkhani za Johannes Rebmann (1820-1876), wamishoni wa Chijeremani amene anakhazikitsa mpingo wa ku Afirika yammawa, komanso anali wokonza wa mtanthauzuramawu woyamba wa Chichewa/ Chinyanja. Mijn naam is Steven Paas, kerk-historicus en onderzoeker van het Chichewa-Chinyanja. Namens de stichting Hart voor Malawi heet ik u welkom op deze website. De site geeft informatie over ons Chichewa/ Chinyanja Woordenboekenproject. We verwachten dat de derde editie van het woordenboek (CE-EC) begin 2012 zal worden gepubliceerd. De site biedt ook een online versie van het woordenboek, die geraadpleegd wordt over de hele wereld. Bovendien is een beschrijving opgenomen van de geschiedenis van het vervaardigen van woordenboeken (lexicografie) in het Chichewa/ Chinyanja. Tenslotte voegden we informatie toe over Johannes Rebmann (1820-1876), Duits zendeling en kerkstichter in Oost Afrika, die het eerste Chichewa/ Chinyanja woordenboek samenstelde. |